Machitidwe 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo anagwa pansi ndipo anamva mawu akumuuza kuti: “Saulo, Saulo n’chifukwa chiyani ukundizunza?”+ Machitidwe 26:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno tonse titagwa pansi, ndinamva mawu akundiuza m’Chiheberi kuti, ‘Saulo, Saulo, n’chifukwa chiyani ukundizunza ine? Ukungovutika popitiriza kuchita ngati nyama imene ikuponya miyendo yake kuti imenye zisonga zotosera.’*+
4 Pamenepo anagwa pansi ndipo anamva mawu akumuuza kuti: “Saulo, Saulo n’chifukwa chiyani ukundizunza?”+
14 Ndiyeno tonse titagwa pansi, ndinamva mawu akundiuza m’Chiheberi kuti, ‘Saulo, Saulo, n’chifukwa chiyani ukundizunza ine? Ukungovutika popitiriza kuchita ngati nyama imene ikuponya miyendo yake kuti imenye zisonga zotosera.’*+