Machitidwe 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Atafika ku Yerusalemu+ anayesetsa kuti agwirizane ndi ophunzira kumeneko. Koma onse ankamuopa, chifukwa sanakhulupirire kuti anali wophunzira. Agalatiya 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiye pambuyo pa zaka zitatu ndinapita ku Yerusalemu+ kukacheza kwa Kefa+ ndipo ndinakhala naye masiku 15.
26 Atafika ku Yerusalemu+ anayesetsa kuti agwirizane ndi ophunzira kumeneko. Koma onse ankamuopa, chifukwa sanakhulupirire kuti anali wophunzira.
18 Ndiye pambuyo pa zaka zitatu ndinapita ku Yerusalemu+ kukacheza kwa Kefa+ ndipo ndinakhala naye masiku 15.