Luka 24:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 inu mudzakhala mboni+ za zimenezi. Machitidwe 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma mzimu woyera ukadzafika pa inu, mudzalandira mphamvu.+ Pamenepo mudzakhala mboni+ zanga mu Yerusalemu,+ ku Yudeya konse ndi ku Samariya,+ mpaka kumalekezero a dziko lapansi.”+ Machitidwe 2:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Yesu ameneyo Mulungu anamuukitsa, ndipo tonsefe ndife mboni za choonadi chimenecho.+
8 Koma mzimu woyera ukadzafika pa inu, mudzalandira mphamvu.+ Pamenepo mudzakhala mboni+ zanga mu Yerusalemu,+ ku Yudeya konse ndi ku Samariya,+ mpaka kumalekezero a dziko lapansi.”+