Genesis 37:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tsopano amuna amalonda achimidiyani+ aja anali kudutsa mumsewu. Pamenepo abale a Yosefe anamutulutsa m’chitsimemo+ n’kumugulitsa kwa Aisimaeliwo. Anamugulitsa ndalama zasiliva 20,+ ndipo iwo anapita naye ku Iguputo. Genesis 45:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo Yosefe anauza abale akewo kuti: “Senderani pafupi ndi ine.” Ndipo anasenderadi pafupi naye. Ndiyeno Yosefe anati: “Ndine m’bale wanu uja Yosefe, amene munamugulitsa ku Iguputo.+ Salimo 105:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mulungu anatsogoza munthu kuti anthu akewo abwere pambuyo pake,Anatumiza Yosefe amene anagulitsidwa kuti akhale kapolo.+
28 Tsopano amuna amalonda achimidiyani+ aja anali kudutsa mumsewu. Pamenepo abale a Yosefe anamutulutsa m’chitsimemo+ n’kumugulitsa kwa Aisimaeliwo. Anamugulitsa ndalama zasiliva 20,+ ndipo iwo anapita naye ku Iguputo.
4 Pamenepo Yosefe anauza abale akewo kuti: “Senderani pafupi ndi ine.” Ndipo anasenderadi pafupi naye. Ndiyeno Yosefe anati: “Ndine m’bale wanu uja Yosefe, amene munamugulitsa ku Iguputo.+
17 Mulungu anatsogoza munthu kuti anthu akewo abwere pambuyo pake,Anatumiza Yosefe amene anagulitsidwa kuti akhale kapolo.+