Yohane 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma mthandiziyo akadzafika, amene ndi mzimu wa choonadi,+ adzakutsogolerani m’choonadi chonse. Pakuti sadzalankhula zongoganiza mwa iye yekha, koma adzalankhula zimene wazimva, ndipo adzalengeza kwa inu zinthu zimene zikubwera.+ Machitidwe 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Petulo ali mkati moganizira za masomphenyawo, mzimu+ unati: “Tamvera! Pali amuna atatu amene akukufuna.
13 Koma mthandiziyo akadzafika, amene ndi mzimu wa choonadi,+ adzakutsogolerani m’choonadi chonse. Pakuti sadzalankhula zongoganiza mwa iye yekha, koma adzalankhula zimene wazimva, ndipo adzalengeza kwa inu zinthu zimene zikubwera.+
19 Petulo ali mkati moganizira za masomphenyawo, mzimu+ unati: “Tamvera! Pali amuna atatu amene akukufuna.