Genesis 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Motero Mulungu analenga munthu m’chifaniziro chake,+ m’chifaniziro cha Mulungu anam’lenga iye. Anawalenga mwamuna ndi mkazi.+
27 Motero Mulungu analenga munthu m’chifaniziro chake,+ m’chifaniziro cha Mulungu anam’lenga iye. Anawalenga mwamuna ndi mkazi.+