Machitidwe 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mulungu atasankha Mtumiki wake, choyamba anamutumiza kwa inu,+ kuti adzakudalitseni mwa kubweza aliyense wa inu kuti musiye ntchito zanu zoipa.”
26 Mulungu atasankha Mtumiki wake, choyamba anamutumiza kwa inu,+ kuti adzakudalitseni mwa kubweza aliyense wa inu kuti musiye ntchito zanu zoipa.”