Yohane 15:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Akadzafika mthandizi amene ndidzamutumiza kuchokera kwa Atate,+ amene ndi mzimu wa choonadi wochokera kwa Atate, ameneyo adzandichitira umboni,+ 1 Akorinto 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano sitinalandire mzimu+ wa dziko, koma mzimu+ wochokera kwa Mulungu, kuti tidziwe zinthu zimene Mulungu watipatsa mokoma mtima.+
26 Akadzafika mthandizi amene ndidzamutumiza kuchokera kwa Atate,+ amene ndi mzimu wa choonadi wochokera kwa Atate, ameneyo adzandichitira umboni,+
12 Tsopano sitinalandire mzimu+ wa dziko, koma mzimu+ wochokera kwa Mulungu, kuti tidziwe zinthu zimene Mulungu watipatsa mokoma mtima.+