Machitidwe 13:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Dziwaninso kuti pa zinthu zonse zimene kunali kosatheka kuti muyesedwe opanda mlandu kudzera m’chilamulo cha Mose,+ aliyense wokhulupirira akuyesedwa wopanda mlandu kudzera mwa Iyeyu.+ Agalatiya 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 N’chifukwa chake Chilamulo chakhala mtsogoleri* wotifikitsa kwa Khristu,+ kuti tiyesedwe olungama+ chifukwa cha chikhulupiriro.
39 Dziwaninso kuti pa zinthu zonse zimene kunali kosatheka kuti muyesedwe opanda mlandu kudzera m’chilamulo cha Mose,+ aliyense wokhulupirira akuyesedwa wopanda mlandu kudzera mwa Iyeyu.+
24 N’chifukwa chake Chilamulo chakhala mtsogoleri* wotifikitsa kwa Khristu,+ kuti tiyesedwe olungama+ chifukwa cha chikhulupiriro.