1 Akorinto 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tisamachite dama,+ mmene ena mwa iwo anachitira dama, n’kufa 23,000 tsiku limodzi.+ Aheberi 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chotero, tiyeni tichite chilichonse chotheka kuti tilowe mu mpumulo umenewo, kuopera kuti wina angagwe ndi kutengera chitsanzo cha kusamvera cha makolo athuwo.+
11 Chotero, tiyeni tichite chilichonse chotheka kuti tilowe mu mpumulo umenewo, kuopera kuti wina angagwe ndi kutengera chitsanzo cha kusamvera cha makolo athuwo.+