Genesis 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo anali kufuula kwa Loti kuti: “Kodi amuna amene abwera usiku uno aja, ali kuti? Atulutse kuti tigone nawo.”+ Levitiko 20:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “‘Mwamuna akagona ndi mwamuna mnzake, mmene mwamuna amagonera ndi mkazi, onse awiri achita chinthu chonyansa.+ Iwo aziphedwa ndithu. Mlandu wa magazi awo ukhale wa iwo eni. 1 Akorinto 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi zoonadi inu simukudziwa kuti anthu osalungama sadzalowa mu ufumu wa Mulungu?+ Musasocheretsedwe. Adama,+ opembedza mafano,+ achigololo,+ amuna amene amagonedwa ndi amuna anzawo,+ amuna ogona amuna anzawo,+
5 Iwo anali kufuula kwa Loti kuti: “Kodi amuna amene abwera usiku uno aja, ali kuti? Atulutse kuti tigone nawo.”+
13 “‘Mwamuna akagona ndi mwamuna mnzake, mmene mwamuna amagonera ndi mkazi, onse awiri achita chinthu chonyansa.+ Iwo aziphedwa ndithu. Mlandu wa magazi awo ukhale wa iwo eni.
9 Kodi zoonadi inu simukudziwa kuti anthu osalungama sadzalowa mu ufumu wa Mulungu?+ Musasocheretsedwe. Adama,+ opembedza mafano,+ achigololo,+ amuna amene amagonedwa ndi amuna anzawo,+ amuna ogona amuna anzawo,+