Afilipi 2:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chotero, mulandireni monga mwa nthawi zonse,+ mwa Ambuye ndi chimwemwe chonse. Ndipo abale okhala ngati iyeyu muziwalemekeza kwambiri,+ 3 Yohane 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho, ife tili ndi udindo wolandira bwino anthu amenewa ndi kuwachereza,+ kuti akhale antchito anzathu m’choonadi.+
29 Chotero, mulandireni monga mwa nthawi zonse,+ mwa Ambuye ndi chimwemwe chonse. Ndipo abale okhala ngati iyeyu muziwalemekeza kwambiri,+
8 Choncho, ife tili ndi udindo wolandira bwino anthu amenewa ndi kuwachereza,+ kuti akhale antchito anzathu m’choonadi.+