1 Akorinto 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiponso, munthu aliyense wochita nawo mpikisano amakhala wodziletsa+ pa zinthu zonse. Iwo amachita zimenezo kuti apeze nkhata ya kumutu imene imawonongeka,+ koma ife, kuti tikapeze nkhata ya kumutu yosakhoza kuwonongeka.+
25 Ndiponso, munthu aliyense wochita nawo mpikisano amakhala wodziletsa+ pa zinthu zonse. Iwo amachita zimenezo kuti apeze nkhata ya kumutu imene imawonongeka,+ koma ife, kuti tikapeze nkhata ya kumutu yosakhoza kuwonongeka.+