Yobu 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Amachititsa alangizi kuyenda opanda nsapato,+Ndipo oweruza amawachititsa misala. Aroma 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ngakhale anali kunena motsimikiza kuti ndi anzeru, iwo anakhala opusa+