Yuda 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiponso angelo amene sanasunge malo awo oyambirira koma anasiya malo awo okhala,+ Mulungu anawasunga kosatha m’maunyolo,+ mu mdima wandiweyani kuti adzaweruzidwe pa tsiku lalikulu.+
6 Ndiponso angelo amene sanasunge malo awo oyambirira koma anasiya malo awo okhala,+ Mulungu anawasunga kosatha m’maunyolo,+ mu mdima wandiweyani kuti adzaweruzidwe pa tsiku lalikulu.+