1 Akorinto 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mwachitsanzo, mwa mzimu wina amapatsidwa mawu anzeru,+ ndipo wina amapatsidwa mawu ozindikira+ mwa mzimu womwewo. 2 Akorinto 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ngati ndilibe luso la kulankhula,+ si kuti ndine wosadziwanso zinthu.+ Koma m’njira iliyonse tinakusonyezani kuti ndife odziwa zinthu pa zonse.+
8 Mwachitsanzo, mwa mzimu wina amapatsidwa mawu anzeru,+ ndipo wina amapatsidwa mawu ozindikira+ mwa mzimu womwewo.
6 Ngati ndilibe luso la kulankhula,+ si kuti ndine wosadziwanso zinthu.+ Koma m’njira iliyonse tinakusonyezani kuti ndife odziwa zinthu pa zonse.+