Salimo 119:99 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 99 Ndakhala wozindikira kwambiri kuposa aphunzitsi anga,+Chifukwa ndimasinkhasinkha zikumbutso zanu.+ Aefeso 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inde, kuti tisakhalenso tiana, otengekatengeka+ ngati kuti tikukankhidwa ndi mafunde, ndiponso otengeka kupita uku ndi uku ndi mphepo iliyonse ya chiphunzitso+ chonyenga+ cha anthu, mwa kuchenjera kwa anthu popeka mabodza. Aheberi 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti aliyense woyamwa mkaka sadziwa mawu a chilungamo, chifukwa adakali kamwana.+
99 Ndakhala wozindikira kwambiri kuposa aphunzitsi anga,+Chifukwa ndimasinkhasinkha zikumbutso zanu.+
14 Inde, kuti tisakhalenso tiana, otengekatengeka+ ngati kuti tikukankhidwa ndi mafunde, ndiponso otengeka kupita uku ndi uku ndi mphepo iliyonse ya chiphunzitso+ chonyenga+ cha anthu, mwa kuchenjera kwa anthu popeka mabodza.