Machitidwe 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 mpaka tsiku limene anatengedwa kupita kumwamba,+ atapereka malangizo kudzera mwa mzimu woyera kwa atumwi amene iye anawasankha.+ Machitidwe 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano atasonkhana pamodzi, anayamba kumufunsa kuti: “Ambuye, kodi mubwezeretsa ufumu+ kwa Isiraeli pa nthawi ino?”
2 mpaka tsiku limene anatengedwa kupita kumwamba,+ atapereka malangizo kudzera mwa mzimu woyera kwa atumwi amene iye anawasankha.+
6 Tsopano atasonkhana pamodzi, anayamba kumufunsa kuti: “Ambuye, kodi mubwezeretsa ufumu+ kwa Isiraeli pa nthawi ino?”