Afilipi 2:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chotero, mulandireni monga mwa nthawi zonse,+ mwa Ambuye ndi chimwemwe chonse. Ndipo abale okhala ngati iyeyu muziwalemekeza kwambiri,+ 1 Atesalonika 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano tikukupemphani abale, kuti muzilemekeza anthu amene akugwira ntchito mwakhama pakati panu, amenenso amakutsogolerani+ mwa Ambuye ndi kukulangizani. 1 Timoteyo 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Akulu otsogolera+ bwino apatsidwe ulemu waukulu,+ makamaka amene amachita khama kulankhula ndi kuphunzitsa.+
29 Chotero, mulandireni monga mwa nthawi zonse,+ mwa Ambuye ndi chimwemwe chonse. Ndipo abale okhala ngati iyeyu muziwalemekeza kwambiri,+
12 Tsopano tikukupemphani abale, kuti muzilemekeza anthu amene akugwira ntchito mwakhama pakati panu, amenenso amakutsogolerani+ mwa Ambuye ndi kukulangizani.
17 Akulu otsogolera+ bwino apatsidwe ulemu waukulu,+ makamaka amene amachita khama kulankhula ndi kuphunzitsa.+