1 Petulo 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atamandike Mulungu amenenso ndi Atate wa Ambuye wathu Yesu Khristu,+ pakuti mwachifundo chake chachikulu, anatibereka mwatsopano+ kuti tikhale ndi chiyembekezo cha moyo+ mwa kuukitsidwa+ kwa Yesu Khristu.
3 Atamandike Mulungu amenenso ndi Atate wa Ambuye wathu Yesu Khristu,+ pakuti mwachifundo chake chachikulu, anatibereka mwatsopano+ kuti tikhale ndi chiyembekezo cha moyo+ mwa kuukitsidwa+ kwa Yesu Khristu.