Aefeso 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 ndi kuvala+ umunthu watsopano+ umene unalengedwa+ mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu ndipo umatsatira zofunika pa chilungamo chenicheni+ ndi pa kukhulupirika. Aefeso 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chotero muzitsanzira Mulungu,+ monga ana ake okondedwa,
24 ndi kuvala+ umunthu watsopano+ umene unalengedwa+ mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu ndipo umatsatira zofunika pa chilungamo chenicheni+ ndi pa kukhulupirika.