Agalatiya 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo ngakhale Tito,+ amene ndinali naye limodzi, sanafunikire kudulidwa,+ ngakhale kuti iye ndi Mgiriki. Tito 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndikulembera Tito, mwana wanga+ weniweni m’chikhulupiriro chimodzi chomwe tili nacho: Kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere wa Mulungu Atate+ ndi Khristu Yesu Mpulumutsi wathu,+ zikhale nawe.
3 Ndipo ngakhale Tito,+ amene ndinali naye limodzi, sanafunikire kudulidwa,+ ngakhale kuti iye ndi Mgiriki.
4 Ndikulembera Tito, mwana wanga+ weniweni m’chikhulupiriro chimodzi chomwe tili nacho: Kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere wa Mulungu Atate+ ndi Khristu Yesu Mpulumutsi wathu,+ zikhale nawe.