Yohane 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mthandizi ameneyo ndi mzimu wa choonadi.+ Mzimu umenewo dziko silingaulandire,+ chifukwa siliuona kapena kuudziwa. Inu mumaudziwa chifukwa umakhala mwa inu, ndipo uli mwa inu.+
17 Mthandizi ameneyo ndi mzimu wa choonadi.+ Mzimu umenewo dziko silingaulandire,+ chifukwa siliuona kapena kuudziwa. Inu mumaudziwa chifukwa umakhala mwa inu, ndipo uli mwa inu.+