Aroma 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma tsopano tamasulidwa ku Chilamulo,+ chifukwa tafa+ ku chilamulo chimene chinali kutimanga chija, kuti tikhale akapolo+ m’njira yatsopano motsogoleredwa ndi mzimu,+ osati m’njira yakale motsogoleredwa ndi malamulo olembedwa.+
6 Koma tsopano tamasulidwa ku Chilamulo,+ chifukwa tafa+ ku chilamulo chimene chinali kutimanga chija, kuti tikhale akapolo+ m’njira yatsopano motsogoleredwa ndi mzimu,+ osati m’njira yakale motsogoleredwa ndi malamulo olembedwa.+