4 Chifukwa panopa wina akabwera kwa inu n’kulalikira za Yesu wosiyana ndi amene tinamulalikira,+ kapena wina akakubweretserani mzimu wosiyana ndi umene munalandira kale,+ kapena uthenga wabwino+ wosiyana ndi umene munaulandira, inu mumangomulolera munthu woteroyo.+