Aroma 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma tsopano tamasulidwa ku Chilamulo,+ chifukwa tafa+ ku chilamulo chimene chinali kutimanga chija, kuti tikhale akapolo+ m’njira yatsopano motsogoleredwa ndi mzimu,+ osati m’njira yakale motsogoleredwa ndi malamulo olembedwa.+ Agalatiya 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Khristu anatimasula kuti tikhale ndi ufulu umenewu.+ Chotero khalani olimba,+ ndipo musalole kumangidwanso m’goli laukapolo.+
6 Koma tsopano tamasulidwa ku Chilamulo,+ chifukwa tafa+ ku chilamulo chimene chinali kutimanga chija, kuti tikhale akapolo+ m’njira yatsopano motsogoleredwa ndi mzimu,+ osati m’njira yakale motsogoleredwa ndi malamulo olembedwa.+
5 Khristu anatimasula kuti tikhale ndi ufulu umenewu.+ Chotero khalani olimba,+ ndipo musalole kumangidwanso m’goli laukapolo.+