Miyambo 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ngakhale mnyamata amadziwika ndi ntchito zake, ngati zochita zake zili zoyera ndiponso zowongoka.+ 1 Akorinto 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 chifukwa mukadali anthu oganiza ngati anthu a m’dzikoli.*+ Kodi ngati mukuchitirana nsanje ndi kukangana nokhanokha,+ sindiye kuti ndinu akuthupi ndipo mukuyenda monga anthu?+
11 Ngakhale mnyamata amadziwika ndi ntchito zake, ngati zochita zake zili zoyera ndiponso zowongoka.+
3 chifukwa mukadali anthu oganiza ngati anthu a m’dzikoli.*+ Kodi ngati mukuchitirana nsanje ndi kukangana nokhanokha,+ sindiye kuti ndinu akuthupi ndipo mukuyenda monga anthu?+