Luka 16:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma Abulahamu anati, ‘Mwanawe, kumbukira kuti unalandiriratu zabwino zako zonse pamene unali moyo, ndipo Lazaro analandiriratu zinthu zoipa. Koma tsopano akusangalala kuno ndipo iwe ukuzunzika.+ Aroma 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzaweruza aliyense malinga ndi ntchito zake motere:+
25 Koma Abulahamu anati, ‘Mwanawe, kumbukira kuti unalandiriratu zabwino zako zonse pamene unali moyo, ndipo Lazaro analandiriratu zinthu zoipa. Koma tsopano akusangalala kuno ndipo iwe ukuzunzika.+