1 Akorinto 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti mofanana ndi thupi lomwe ndi limodzi koma lili ndi ziwalo zambiri, ndipo ziwalo zonse za thupi, ngakhale ndi zambiri, zimapanga thupi limodzi,+ ndi mmenenso Khristu alili.+
12 Pakuti mofanana ndi thupi lomwe ndi limodzi koma lili ndi ziwalo zambiri, ndipo ziwalo zonse za thupi, ngakhale ndi zambiri, zimapanga thupi limodzi,+ ndi mmenenso Khristu alili.+