Akolose 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 tsopano wagwirizana+ nanunso pogwiritsa ntchito thupi lanyama la mwanayo kudzera mu imfa yake.+ Wachita izi kuti akuperekeni pamaso pa iyeyo, muli opatulika ndi opanda chilema,+ ndiponso opanda chifukwa chokunenezerani.+
22 tsopano wagwirizana+ nanunso pogwiritsa ntchito thupi lanyama la mwanayo kudzera mu imfa yake.+ Wachita izi kuti akuperekeni pamaso pa iyeyo, muli opatulika ndi opanda chilema,+ ndiponso opanda chifukwa chokunenezerani.+