Machitidwe 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno Petulo anawauza kuti: “Inunso mukudziwa bwino kuti n’kosaloleka kuti Myuda azicheza ndi munthu wa fuko lina kapena kumuyandikira.+ Koma tsopano Mulungu wandionetsa kuti ndisatchule munthu aliyense kuti woipitsidwa kapena wonyansa.+
28 Ndiyeno Petulo anawauza kuti: “Inunso mukudziwa bwino kuti n’kosaloleka kuti Myuda azicheza ndi munthu wa fuko lina kapena kumuyandikira.+ Koma tsopano Mulungu wandionetsa kuti ndisatchule munthu aliyense kuti woipitsidwa kapena wonyansa.+