Zekariya 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno udzamuuze kuti,“‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Munthu uyu+ dzina lake ndi Mphukira.+ Adzaphuka pamalo ake ndipo adzamanga kachisi wa Yehova.+ 1 Akorinto 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kodi inu simukudziwa kuti ndinu kachisi wa Mulungu,+ ndi kuti mzimu wa Mulungu ukukhala mwa inu?+ 1 Akorinto 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kodi zoona inu simukudziwa kuti thupi lanu ndilo kachisi+ wa mzimu woyera umene uli mwa inu,+ umene munapatsidwa ndi Mulungu? Ndiponso mwiniwake wa inuyo si inu,+
12 Ndiyeno udzamuuze kuti,“‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Munthu uyu+ dzina lake ndi Mphukira.+ Adzaphuka pamalo ake ndipo adzamanga kachisi wa Yehova.+
19 Kodi zoona inu simukudziwa kuti thupi lanu ndilo kachisi+ wa mzimu woyera umene uli mwa inu,+ umene munapatsidwa ndi Mulungu? Ndiponso mwiniwake wa inuyo si inu,+