Yohane 17:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ine wogwirizana ndi iwo, inu wogwirizana ndi ine, kuti iwo akhale mu umodzi weniweni,+ kuti dziko lidziwe kuti inu munandituma ine, ndi kuti munawakonda iwo mmene munandikondera ine.
23 Ine wogwirizana ndi iwo, inu wogwirizana ndi ine, kuti iwo akhale mu umodzi weniweni,+ kuti dziko lidziwe kuti inu munandituma ine, ndi kuti munawakonda iwo mmene munandikondera ine.