Yohane 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo Yesu analankhula nawonso kuti: “Ine ndine kuwala+ kwa dziko. Wonditsatira ine sadzayenda mumdima,+ koma adzakhala nako kuwala kwa moyo.” 2 Timoteyo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma tsopano izi zatsimikizirika bwino chifukwa cha kuonekera+ kwa Mpulumutsi wathu Khristu Yesu, amene wathetsa mphamvu imfa.+ Kudzera mu uthenga wabwino,+ iye watidziwitsa bwinobwino+ mmene tingapezere moyo+ wosawonongeka.+
12 Pamenepo Yesu analankhula nawonso kuti: “Ine ndine kuwala+ kwa dziko. Wonditsatira ine sadzayenda mumdima,+ koma adzakhala nako kuwala kwa moyo.”
10 Koma tsopano izi zatsimikizirika bwino chifukwa cha kuonekera+ kwa Mpulumutsi wathu Khristu Yesu, amene wathetsa mphamvu imfa.+ Kudzera mu uthenga wabwino,+ iye watidziwitsa bwinobwino+ mmene tingapezere moyo+ wosawonongeka.+