1 Akorinto 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano sitinalandire mzimu+ wa dziko, koma mzimu+ wochokera kwa Mulungu, kuti tidziwe zinthu zimene Mulungu watipatsa mokoma mtima.+ Yakobo 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kapena mukuyesa kuti lemba limanena pachabe kuti: “Mzimu umene uli mwa ife uli ndi chizolowezi cholakalaka zinthu zosiyanasiyana”?+
12 Tsopano sitinalandire mzimu+ wa dziko, koma mzimu+ wochokera kwa Mulungu, kuti tidziwe zinthu zimene Mulungu watipatsa mokoma mtima.+
5 Kapena mukuyesa kuti lemba limanena pachabe kuti: “Mzimu umene uli mwa ife uli ndi chizolowezi cholakalaka zinthu zosiyanasiyana”?+