Salimo 145:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova amakomera mtima aliyense,+Ndipo ntchito zake zonse amazichitira chifundo.+ Yesaya 54:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti mapiri akhoza kuchotsedwa, ndipo zitunda zikhoza kugwedezeka,+ koma kukoma mtima kwanga kosatha sikudzachotsedwa kwa iwe,+ ndipo pangano langa la mtendere silidzagwedezeka,”+ watero Yehova, amene akukuchitira chifundo.+ Aroma 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Palibe kusiyana pakati pa Myuda ndi Mgiriki,+ popeza kwa onsewo Ambuye ndi mmodzi, amene amapereka mowolowa manja+ kwa onse oitana pa dzina lake.
10 Pakuti mapiri akhoza kuchotsedwa, ndipo zitunda zikhoza kugwedezeka,+ koma kukoma mtima kwanga kosatha sikudzachotsedwa kwa iwe,+ ndipo pangano langa la mtendere silidzagwedezeka,”+ watero Yehova, amene akukuchitira chifundo.+
12 Palibe kusiyana pakati pa Myuda ndi Mgiriki,+ popeza kwa onsewo Ambuye ndi mmodzi, amene amapereka mowolowa manja+ kwa onse oitana pa dzina lake.