2 Akorinto 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano amene anatikonzekeretsa kuti tilandire zimenezi ndi Mulungu.+ Iye ndiye anatipatsa chikole+ cha zinthu zam’tsogolo, chomwe ndi mzimu.+
5 Tsopano amene anatikonzekeretsa kuti tilandire zimenezi ndi Mulungu.+ Iye ndiye anatipatsa chikole+ cha zinthu zam’tsogolo, chomwe ndi mzimu.+