Aroma 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Amenewa ndi Aisiraeli,+ amene Mulungu anawatenga kukhala ana ake.+ Anawapatsanso ulemerero,+ mapangano,+ Chilamulo,+ utumiki wopatulika+ ndi malonjezo.+
4 Amenewa ndi Aisiraeli,+ amene Mulungu anawatenga kukhala ana ake.+ Anawapatsanso ulemerero,+ mapangano,+ Chilamulo,+ utumiki wopatulika+ ndi malonjezo.+