Salimo 145:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehova ali pafupi ndi onse oitanira pa iye.+Iye ali pafupi ndi onse amene amamuitana m’choonadi,+ Yohane 16:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pa tsiku limenelo+ simudzandifunsanso mafunso. Ndithudi ndikukuuzani, Ngati mupempha chilichonse+ kwa Atate m’dzina langa adzakupatsani.+
23 Pa tsiku limenelo+ simudzandifunsanso mafunso. Ndithudi ndikukuuzani, Ngati mupempha chilichonse+ kwa Atate m’dzina langa adzakupatsani.+