Aroma 8:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti tinapulumutsidwa tili ndi chiyembekezo chimenechi,+ koma chimene chikuyembekezedwa chikaoneka sichikhalanso choyembekezedwa, chifukwa munthu akaona chinthu chimene anali kuchiyembekezera, kodi amachiyembekezanso?
24 Pakuti tinapulumutsidwa tili ndi chiyembekezo chimenechi,+ koma chimene chikuyembekezedwa chikaoneka sichikhalanso choyembekezedwa, chifukwa munthu akaona chinthu chimene anali kuchiyembekezera, kodi amachiyembekezanso?