1 Akorinto 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiye chifukwa chake, okondedwa anga, thawani+ kupembedza mafano.+ 1 Akorinto 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mukudziwa kuti pamene munali a mitundu ina,+ munali kutsogoleredwa m’njira zosiyanasiyana ku mafano+ osalankhula.+ Agalatiya 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngakhale zili choncho, pamene munali osadziwa Mulungu,+ munali akapolo a zinthu zimene mwachilengedwe si milungu.+ 1 Yohane 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu ana okondedwa, pewani mafano.+
2 Mukudziwa kuti pamene munali a mitundu ina,+ munali kutsogoleredwa m’njira zosiyanasiyana ku mafano+ osalankhula.+
8 Ngakhale zili choncho, pamene munali osadziwa Mulungu,+ munali akapolo a zinthu zimene mwachilengedwe si milungu.+