Akolose 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Epafura,+ amene anachokera pakati panu, kapolo wa Khristu Yesu, akuti moni. Iye amakupemphererani mwakhama nthawi zonse, kuti pomalizira pake mukhale okhwima mwauzimu+ ndi osakayika ngakhale pang’ono za chifuniro chonse cha Mulungu.
12 Epafura,+ amene anachokera pakati panu, kapolo wa Khristu Yesu, akuti moni. Iye amakupemphererani mwakhama nthawi zonse, kuti pomalizira pake mukhale okhwima mwauzimu+ ndi osakayika ngakhale pang’ono za chifuniro chonse cha Mulungu.