2 Akorinto 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakuti Mwana wa Mulungu,+ Khristu Yesu, amene analalikidwa pakati panu kudzera mwa ineyo, Silivano, ndi Timoteyo,+ sanakhale Inde kenako Ayi, koma mwa iye, Inde wakhalabe Inde.+
19 Pakuti Mwana wa Mulungu,+ Khristu Yesu, amene analalikidwa pakati panu kudzera mwa ineyo, Silivano, ndi Timoteyo,+ sanakhale Inde kenako Ayi, koma mwa iye, Inde wakhalabe Inde.+