Machitidwe 20:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndipo pakati panu anthu ena adzayamba kulankhula zinthu zopotoka+ kuti apatutse ophunzira aziwatsatira.+ 2 Timoteyo 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma pewa nkhani zopeka zimene zimaipitsa zinthu zoyera,+ pakuti kusaopa Mulungu kudzachulukirachulukira+ mwa anthu olankhula zotero, 2 Petulo 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Komanso chifukwa chosirira mwansanje, adzakudyerani masuku pamutu ndi mawu achinyengo.+ Koma chiweruzo chawo chimene chinagamulidwa kalekale+ chikubwera mofulumira, ndipo chiwonongeko chawo sichikuzengereza.+
30 Ndipo pakati panu anthu ena adzayamba kulankhula zinthu zopotoka+ kuti apatutse ophunzira aziwatsatira.+
16 Koma pewa nkhani zopeka zimene zimaipitsa zinthu zoyera,+ pakuti kusaopa Mulungu kudzachulukirachulukira+ mwa anthu olankhula zotero,
3 Komanso chifukwa chosirira mwansanje, adzakudyerani masuku pamutu ndi mawu achinyengo.+ Koma chiweruzo chawo chimene chinagamulidwa kalekale+ chikubwera mofulumira, ndipo chiwonongeko chawo sichikuzengereza.+