Afilipi 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho, pokhala wotsimikiza za chimenechi, ndikudziwa kuti ndikhalabe ndi moyo.+ Chotero ndidzakhala ndi inu nonse kuti mupite patsogolo,+ ndi kuti musangalale pa chikhulupiriro chanu.
25 Choncho, pokhala wotsimikiza za chimenechi, ndikudziwa kuti ndikhalabe ndi moyo.+ Chotero ndidzakhala ndi inu nonse kuti mupite patsogolo,+ ndi kuti musangalale pa chikhulupiriro chanu.