Miyambo 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zachinyengo ndi mawu onama muwaike kutali ndi ine.+ Musandipatse umphawi kapena chuma.+ Ndidye chakudya chimene ndikufunika kudya,+ Aheberi 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Moyo wanu ukhale wosakonda ndalama,+ koma mukhale okhutira+ ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Pakuti Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pang’ono.”+
8 Zachinyengo ndi mawu onama muwaike kutali ndi ine.+ Musandipatse umphawi kapena chuma.+ Ndidye chakudya chimene ndikufunika kudya,+
5 Moyo wanu ukhale wosakonda ndalama,+ koma mukhale okhutira+ ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Pakuti Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pang’ono.”+