Aroma 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kuoneka wolungama pamaso pa Mulungu kumeneku kungatheke mwa kukhulupirira Yesu Khristu,+ ndipo ndi kotheka kwa onse okhala ndi chikhulupiriro.+ Popeza palibe kusiyanitsa.+ Agalatiya 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti kwa Khristu Yesu, kudulidwa kapena kusadulidwa zilibe phindu,+ koma chikhulupiriro+ chimene chimagwira ntchito kudzera m’chikondi.+
22 Kuoneka wolungama pamaso pa Mulungu kumeneku kungatheke mwa kukhulupirira Yesu Khristu,+ ndipo ndi kotheka kwa onse okhala ndi chikhulupiriro.+ Popeza palibe kusiyanitsa.+
6 Pakuti kwa Khristu Yesu, kudulidwa kapena kusadulidwa zilibe phindu,+ koma chikhulupiriro+ chimene chimagwira ntchito kudzera m’chikondi.+