2 Akorinto 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 olankhula zoona, ndiponso okhala ndi mphamvu ya Mulungu.+ Komanso, tikuchita zimenezi ponyamula zida+ za chilungamo kudzanja lamanja ndi lamanzere, Afilipi 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pa zinthu zonse, ndimapeza mphamvu kuchokera kwa iye amene amandipatsa mphamvu.+ Akolose 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tikupemphereranso kuti mulandire mphamvu zazikulu chifukwa cha mphamvu zake zaulemerero,+ kuti muthe kupirira+ zinthu zonse ndi kukhala oleza mtima ndiponso achimwemwe, 1 Petulo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 inuyo amene Mulungu akukutetezani ndi mphamvu yake chifukwa muli ndi chikhulupiriro.+ Mulungu akukutetezani kuti mudzalandire chipulumutso,+ ndipo chipulumutso chimenechi chidzaonekera+ mu nthawi ya mapeto.+
7 olankhula zoona, ndiponso okhala ndi mphamvu ya Mulungu.+ Komanso, tikuchita zimenezi ponyamula zida+ za chilungamo kudzanja lamanja ndi lamanzere,
11 Tikupemphereranso kuti mulandire mphamvu zazikulu chifukwa cha mphamvu zake zaulemerero,+ kuti muthe kupirira+ zinthu zonse ndi kukhala oleza mtima ndiponso achimwemwe,
5 inuyo amene Mulungu akukutetezani ndi mphamvu yake chifukwa muli ndi chikhulupiriro.+ Mulungu akukutetezani kuti mudzalandire chipulumutso,+ ndipo chipulumutso chimenechi chidzaonekera+ mu nthawi ya mapeto.+