Salimo 119:101 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 101 Ndaletsa mapazi anga kuyenda m’njira iliyonse yoipa.+Ndachita izi kuti ndisunge mawu anu.+ 2 Timoteyo 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kapolo wa Ambuye sayenera kukangana ndi anthu,+ koma ayenera kukhala wodekha kwa onse.+ Ayeneranso kukhala woyenerera kuphunzitsa,+ wougwira mtima pokumana ndi zoipa,+ Yakobo 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi pakati panu pali aliyense wanzeru ndi womvetsa zinthu? Ameneyo ayenera kukhala ndi khalidwe labwino limene limasonyeza kuti amachita chilichonse+ mofatsa ndipo kufatsa kwake kumachokera mu nzeru.
24 Kapolo wa Ambuye sayenera kukangana ndi anthu,+ koma ayenera kukhala wodekha kwa onse.+ Ayeneranso kukhala woyenerera kuphunzitsa,+ wougwira mtima pokumana ndi zoipa,+
13 Kodi pakati panu pali aliyense wanzeru ndi womvetsa zinthu? Ameneyo ayenera kukhala ndi khalidwe labwino limene limasonyeza kuti amachita chilichonse+ mofatsa ndipo kufatsa kwake kumachokera mu nzeru.