Yobu 31:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiye ndingatani Mulungu akaimirira,Ndipo akandifunsa ndingamuyankhe chiyani?+ Machitidwe 17:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ m’chilungamo dziko lapansi kumene kuli anthu, kudzera mwa munthu amene iye wamuika. Ndipo wapereka chitsimikizo kwa anthu onse mwa kumuukitsa+ kwa akufa.” Aroma 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zimenezi zidzaonekera pa tsiku limene Mulungu, kudzera mwa Khristu Yesu, adzaweruze+ zinthu zobisika+ za anthu,+ mogwirizana ndi uthenga wabwino umene ndikulengeza.+ Aroma 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chotero aliyense wa ife adzayankha yekha kwa Mulungu.+
31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ m’chilungamo dziko lapansi kumene kuli anthu, kudzera mwa munthu amene iye wamuika. Ndipo wapereka chitsimikizo kwa anthu onse mwa kumuukitsa+ kwa akufa.”
16 Zimenezi zidzaonekera pa tsiku limene Mulungu, kudzera mwa Khristu Yesu, adzaweruze+ zinthu zobisika+ za anthu,+ mogwirizana ndi uthenga wabwino umene ndikulengeza.+